
Mundikumbuke 歌詞
Mundikumbuke - Alick Macheso/Orchestra Mberikwazvo
Mundikumbuke amayi ndasara ndekha
Mundikumbuke amayi ndasara ndekha ine
Mundikumbuke amayi ndasara ndekha
Mundikumbuke amayi ndasara ndekha
Mundikumbuke amayi ndasara ndekha
Mundikumbuke amayi ndasara ndekhaaaaa
Amayi asanafe anasiya mau
Amayi asanafe eeh anasiya mau
Usafunefune moyenda bambo ulinawo
Usafunefune moyenda bambo ulinawo
Usafunefune moyenda bambo ulinawo
Usafunefune moyenda bambo ulinawooooo
Ndine mwana wapatchire
Okula ndi amayi
Ndine mwana wapatchire ine
Okula ndi amayi
Ndine mwana wamasiye
Okulira mu umphawi
Ndine mwana wamasiye
Okulira mu umphawi
Ndine mwana wamasiye ine
Okulira mu umphawi
Ndine mwana wamasiye ine
Okulira mu umphawiiiii
Azimayi achiwiri ana amasiye
Mverani
Azimayi achiwiri ana amasiye
Apatsopeni monga ana anuso
Apatsopeni monga ana anuso
Osataya
Apatsopeni eeh monga ana anuso
Apatsopeni eeh monga ana anuso
Chifundo
Ndili ndi chifundo ine
Chifundo
Ndili ndi chifundo ine
Mavuto
Ndili ndi mavuto ine
Mavuto
Ndili ndi mavuto ine
Amayi anandileraan amwalira kale
Amayi anandilera ine
Anamwalira kale
Poyenda ndimangolira
Kukumbuka ondibala
Poyenda ndimangolira ine
Kukumbuka ondibara
Pogona ndi misonzi chabe
Bambo anga muli kuti inu
Pogona ndi misonzi chabe
Bambo anga muli kuti inu
Ndakulira mu umphawi
Opanda chisoni ndithu
Ndakulira mu umphawi
Opanda chisoni ndithu
Ngati muli ndi umoyo
Kapena munamwalira
Ngati mili ndi umoyo
Kapena munamwalira
Bwanji osabwera Ku tulo
Kapena ndingakondwereko
Bwanji osabwera Ku tulo
Kapena ndingakondwereko
Chifundo
Ndili ndi chifundo ine
Chifundo
Ndili ndi chifundo ine
Mavuto
Ndili ndi mavuto ine
Mavuto
Ndili ndi mavuto ine
Achisale
Mwayenela
Mayooo Mayooo