Lirik Linny Hoo (Explicit)
Linny Hoo (Explicit) - DJ Dr. IcE/Gidess C
Lyrics by:Gidess/Dj Dr. Ice
Composed by:Gidess/Dj Dr. Ice
Linny hoo Linny hoo
Uyu Linny lero mwana amenenyu mwana wa nzeru
Linny hoo
Linny
Linny hoo
Uyu Linny lero mwana amenenyu mwana wa nzeru
Kukacha m'mamawa aah aah
Amatenga tsache
Kusetsa pakhomo pakhomo pa mayi wache
Kukacha m'mamawa
Early morning
Amatenga tsache
Kusetsa pakhomo pakhomo la mayi wache
Makolo a Linny
Ati makolo a Linny
Amuyamikira
Akuti Linny lero mwana ameneyu mwana wa nzeru
Makolo a Linny
Makolo a Linny
Amuyamikira
Akuti Linny lero mwana ameneyu mwana wa nzeru
Linny
Linny
Linny hoo
Linny hoo
Uyu Linny lero mwana amenenyu mwana wa nzeru
Ta nti tinde
Ohh
Kititingidi
Ehmmm
Tinta linta nta nta
Ohoo
Ta nti ti nta nta
Ehmmm
Kidi nkidi nta nta
Oh wooo
Ti nti nkidi ntite
Ohoo woo
Ti nta ti nta nta nta
Ehmmm
Ta nti ti nta nta Linny hoo
Linny
Linny hoo
Uyu Linny lero mwana amenenyu mwana wa nzeru
Agide gogo wa Namadingo
Gide gogo wa Namadingo
Ndamuyamikira kuti Namadingo mwana ameneyu
Hehehe
Mwana wa nzeru
Agide gogo wa Namadingo ndamuyamikira
Kuti Namadingo mwana ameneyu
Mwana wa nzeru
Simukunamana agogo
Nthawi zina ine
Nthawi zina
Ndimalota ine
Bambo anga atandisiya ndatsala ndekha
Nthawi zina ine
Nthawi zina ine
Ndimalota ine bambo anga atamwalira ndasala ndekha
Nkhondo amama
Nkhondo amama
Nkhondo une mama mwee
Nkhondo amama mwe
Iiih nkhondo amama Chalamanda
Uzafera moyoenda we
Nkondo amama
Ihh nkhondo une mama mwee
Ihh
Nkhondo mama Chalamanda uzafera moyoenda we
Ndangomwa mbiriyo mbiriyo mbiritu mwaona lero
Ndangomwa mbiriyo ka mbiriyo mbiritu mwaona lero
Agiddessi ayimba eeh ayimba eeh
Zokomatu mwaona lero
Ndipo Chalamanda
Ayimba eeh ayimba eeh zokomatu mwaona lero
Ndinamva kuti mwakwatira
Mwabala mwana woyera
Dzina lake Musolo eeh
Munamva kwa ndani kuti mwakwatira
Ndamwa kuti mwakwatira
Mwabala mwana oyera
Dzina lake Musolo eeh
Nnangopanga unkhoswe ukwati uzakuzitanani
Musolo eeh
Ati Musolo ehh
Musolo eehh Musolo mayi
Musolo eehh Musolo eh Musolo mayi
Mwana ameneyi ndi mayi ake
Ndikufuna ndipite nawo
Mupite nawo kuti
Ku UK
Mwana ameneyi ndi mayi ake
Ndikufuna ndipite nawo
Ku UK
Maphunziro onse onsee
Akaphunzire ku UK
Maphunziro onse
Onse aphunzire ku UK
Ndamva agogo ndamva
Koma tiyimbeko Che Meri
Che Meri Kunali Che Meri
Che Meri
Ehmmm
Che Meri
Ehhmm
Che Meri
Kunali Che Meri
Che Meri mama mwe
Iya Meri mwe iya darlie kunali Che Meri
Iiiyooh
Iya Meri mwe iya darlie kunali Che Meri
Tiyimbepo kokoma paja
Iyooh
Iya Meri mwe iya darlie kunali Che Meri
Akafuna kunena nane
Agidesi Agidesi Agidesi Agidesi
Inu abwana tabwerani kuno
Akafuna kunena nane
Chalamanda Chalamanda Chalamanda Chalamanda
Inu abwana tabwerani kuno
Akafuna kunena nane
Agidesi Agidesi Agidesi Agidesi
Inu abwana tabwerani kuno
Zinali choncho nthawi ya Napolo oh
Napolo ohh
Iih wachabe
Napolo iiih wachabe
Napolo
Wachabe
Napolo
Wachabe
Watenga Ingalamu tenga Ingalamu kukataya ku mchenga
Kutuma akaidi kukatola
Pobwera adona nalira mayiwe
Wachabe
Napolo
Wachabe
Napolo
Wachabe
Timalize ndi buffalo soldier
Buffalo Soldier
Buffalo to America
Buffalo Soldier
Buffalo to America
When I was a young boy
I dreamed to there in America
When I was a young boy
Ngati ine ka-young boy
I dreamed to there in America
Oyiyooh oyyiyooh oyioyioyiyooh
Kachikenanso agiddes
Oyiyooh oyyiyooh oyioyioyiyooh
If I had much money
I go to see in America oh ye
If I had much money
I go to see in America
Oyioyioyiyoo
Oyioyioyiyoo
Oyioyioyiyoo
Komaliza Agide
Oyioyioyiyoo
Oyioyioyiyoo
Oyioyioyiyoo
Oyioyioyiyoo
mantap