Ngamila 歌詞
Ngamila - Mumford & Sons/Baaba Maal/The Very Best
Lyrics by:Mumford/Sons/The Very Best
Composed by:Mumford/Sons/The Very Best
Produced by:Mumford/Sons/Johan Hugo
Ngamila yanga ili kuti
Ngamila yanga ili kuti
Ngamila yanga ili kuti
Ngamila yanga ili kuti
Ngamila yanga ili kuti
Ngamila yanga ili kuti
Ngamila yanga ili kuti
Ngamila yanga ili kuti
Umafuna nthawi zonse uvutike moyo wonse
Kufuna zonse zabwino zikhale zako
Ufunefune bwanji sungalikwanitse dzikoli
Mapeto ake ndikunenetsa udzagonje ndiwe
You search all your life
Stealing all you find
And you stare at your own hands
Not the hands they entwine
Pokuti upeze chuma mpakana kukhwima
Kunzunitsa mzi kuwataya ku moto
Kufunsafunsa mudzi Ngamila yanga ili kuti
Chonsecho wakwera ngati wachitila dala
Allo saiero hore uye you want meet go
Med bekli ma
Tine anno saiero what you mind annu nuwa
Der benne ma
Sarilo wasa vaiur nitu der benne ma
Eto horrepaa eur niddo der benne ma
Pokuti upeze chuma mpakana kukhwima
Kunzunitsa mzi kuwataya ku moto
Kufunsafunsa mudzi Ngamila yanga ili kuti
Chonsecho wakwera ngati wachitila dala
You have all you need
When you're held by me
Don't pine for what's not
And whatever will be
You have all you need
When you're held by me
Don't pine for what's not
And whatever will be
Ngamila yanga ili kuti
Ngamila yanga ili kuti
Ngamila yanga ili kuti
Ngamila yanga ili kuti
Ngamila yanga ili kuti
Ngamila yanga ili kuti
Ngamila yanga ili kuti
Ngamila yanga ili kuti